Deuteronomo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azimukwapula zikoti 40. Asapitirire pamenepo, kuopera kuti akapitiriza kumukwapula zikoti zambiri+ anganyazitse m’bale wako pamaso pako.
3 Azimukwapula zikoti 40. Asapitirire pamenepo, kuopera kuti akapitiriza kumukwapula zikoti zambiri+ anganyazitse m’bale wako pamaso pako.