41 Pamene anafika pachimulu cha mchenga m’madzimo, chimene mafunde anali kuchiwomba mbali zonse, ngalawa yawo inatitimira mumchengamo. Kutsogolo kwa ngalawayo kunakanirira pansi osasunthika, ndipo mafunde amphamvu anayamba kuwomba kumbuyo kwake moti inayamba kusweka zidutswazidutswa.+