Ezekieli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+
14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+