Machitidwe 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ife sitingaleke kulankhula zinthu zimene tinaziona ndi kuzimva.”+ 1 Akorinto 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sichikondwera ndi zosalungama,+ koma chimakondwera ndi choonadi.+