Aefeso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi, 1 Petulo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+
11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,
8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+