Machitidwe 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Filipo anapita kumzinda wa Samariya+ ndi kuyamba kulalikira za Khristu kwa anthu akumeneko.