1 Akorinto 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati sindine mtumwi kwa ena, mosakayikira ndine mtumwi kwa inu, popeza ndinu chidindo chotsimikizira+ utumwi wanga mwa Ambuye.
2 Ngati sindine mtumwi kwa ena, mosakayikira ndine mtumwi kwa inu, popeza ndinu chidindo chotsimikizira+ utumwi wanga mwa Ambuye.