-
Aheberi 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pakuti pangano limagwira ntchito ngati wina wafapo, popeza siligwira ntchito nthawi iliyonse pamene munthu wochita naye panganoyo ali ndi moyo.
-