Aroma 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa ngati anthu oumirira kusunga chilamulo ndiwo adzalandire cholowacho, ndiye kuti chikhulupiriro chilibenso ntchito ndipo lonjezo lija lathetsedwa.+
14 Chifukwa ngati anthu oumirira kusunga chilamulo ndiwo adzalandire cholowacho, ndiye kuti chikhulupiriro chilibenso ntchito ndipo lonjezo lija lathetsedwa.+