Machitidwe 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atamva zimenezi, anthuwo anabatizidwa m’dzina la Ambuye Yesu.+ Aroma 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kapena simudziwa kuti tonsefe amene tinabatizidwa ndipo tsopano tili mu mgwirizano ndi Khristu Yesu+ tinabatizidwanso mu imfa yake?+
3 Kapena simudziwa kuti tonsefe amene tinabatizidwa ndipo tsopano tili mu mgwirizano ndi Khristu Yesu+ tinabatizidwanso mu imfa yake?+