Genesis 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Sara anakhala akuona mwana amene Hagara Mwiguputo+ anaberekera Abulahamu akuseka Isaki.+ 2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+