1 Akorinto 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi simukudziwa kuti ochita mpikisano wa liwiro+ amathamanga onse, koma mmodzi yekha ndiye amalandira mphoto?+ Thamangani+ m’njira yoti mukalandire mphotoyo.+ Agalatiya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi ndinu opusa chonchi? Munayamba ndi kudalira mzimu,+ kodi tsopano mukufuna kumaliza ndi kudalira zinthu zochokera kwa anthu opanda ungwiro?+
24 Kodi simukudziwa kuti ochita mpikisano wa liwiro+ amathamanga onse, koma mmodzi yekha ndiye amalandira mphoto?+ Thamangani+ m’njira yoti mukalandire mphotoyo.+
3 Kodi ndinu opusa chonchi? Munayamba ndi kudalira mzimu,+ kodi tsopano mukufuna kumaliza ndi kudalira zinthu zochokera kwa anthu opanda ungwiro?+