3 N’chifukwa chake ndinalemba zimenezi, kuti ndikadzabwera kumeneko, ndisadzakhale wachisoni+ chifukwa cha anthu amene ndiyenera kusangalala nawo.+ Pakuti ndili ndi chikhulupiriro+ mwa nonsenu kuti chimwemwe chimene ndili nacho ndi chimenenso nonsenu muli nacho.