Maliko 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 choncho Afarisi ndi alembi amenewa anam’funsa iye kuti: “N’chifukwa chiyani ophunzira anu satsatira miyambo ya makolo, koma amadya chakudya ndi manja oipitsidwa?”+
5 choncho Afarisi ndi alembi amenewa anam’funsa iye kuti: “N’chifukwa chiyani ophunzira anu satsatira miyambo ya makolo, koma amadya chakudya ndi manja oipitsidwa?”+