Aroma 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ife olimba tiyenera kunyamula zofooka za osalimba,+ osati kumadzikondweretsa tokha ayi.+ 2 Akorinto 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndani ali wofooka,+ ine osakhalanso wofooka? Ndani wakhumudwitsidwa, ine osakwiya nazo? 1 Atesalonika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.
14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.