Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana.+ Yohane 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Lamulo langa ndi ili, mukondane monga mmene inenso ndakukonderani.+ 1 Yohane 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo iye anatipatsa lamulo ili lakuti,+ munthu amene amakonda Mulungu azikondanso m’bale wake.+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana.+