Yobu 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi zingakhale bwino kuti iye akufufuzeni?+Kapena mungam’pusitse ngati mmene mungapusitsire munthu?
9 Kodi zingakhale bwino kuti iye akufufuzeni?+Kapena mungam’pusitse ngati mmene mungapusitsire munthu?