Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chotero, pa nthawi ino alipo ena ochepa+ amene anasankhidwa+ mwa kukoma mtima kwakukulu.

  • 1 Akorinto 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mwa kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, ndili monga ndililimu. Ndipo kukoma mtima kwake kwakukulu kumene anandisonyeza sikunapite pachabe,+ koma ndinagwira ntchito molimbika kuposa atumwi ena onse.+ Ngakhale zili choncho, si mwa ine ndekha ayi, koma kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kumene kuli nane.+

  • Aefeso 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndinakhala mtumiki+ wa zimenezi mogwirizana ndi mphatso yaulere ya kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene ndinapatsidwa mogwirizana ndi mmene mphamvu yake imagwirira ntchito.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena