Machitidwe 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndipo atadya chakudya anapezanso mphamvu.+ Kwa masiku angapo anakhala ndi ophunzira ku Damasiko.+