Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi? 1 Akorinto 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tili ndi ufulu wotenga alongo amene ndi akazi athu+ pa maulendo, mmene amachitira atumwi ena onse ndiponso abale a Ambuye+ komanso Kefa,+ si choncho kodi?
55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?
5 Tili ndi ufulu wotenga alongo amene ndi akazi athu+ pa maulendo, mmene amachitira atumwi ena onse ndiponso abale a Ambuye+ komanso Kefa,+ si choncho kodi?