27 Choncho Baranaba anamuthandiza+ mwa kupita naye kwa atumwi. Kumeneko iye anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Saulo anaonera Ambuye+ amene analankhula naye pamsewu.+ Anawafotokozeranso mmene Saulo analankhulira molimba mtima ku Damasiko+ m’dzina la Yesu.