1 Yohane 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene ali mwana wa Mulungu sapitiriza kuchita tchimo,+ chifukwa mbewu ya Mulungu yopatsa moyo imakhalabe mwa munthu ameneyo, ndipo sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, chifukwa ndi mwana wa Mulungu.+
9 Aliyense amene ali mwana wa Mulungu sapitiriza kuchita tchimo,+ chifukwa mbewu ya Mulungu yopatsa moyo imakhalabe mwa munthu ameneyo, ndipo sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, chifukwa ndi mwana wa Mulungu.+