1 Akorinto 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma tikulankhula za nzeru ya Mulungu imene inaonekera m’chinsinsi chopatulika,+ nzeru yobisika. Mulungu anakonzeratu zochita zimenezi kusanakhale nthawi* zosiyanasiyana,+ kuti tikhale ndi ulemerero. Aefeso 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+
7 Koma tikulankhula za nzeru ya Mulungu imene inaonekera m’chinsinsi chopatulika,+ nzeru yobisika. Mulungu anakonzeratu zochita zimenezi kusanakhale nthawi* zosiyanasiyana,+ kuti tikhale ndi ulemerero.
9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+