Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga+ ndimasangalala kwambiri+ ndi chilamulo cha Mulungu, 2 Akorinto 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho sitikubwerera m’mbuyo. Koma ngakhale munthu wathu wakunja akutha, ndithudi munthu wathu wamkati+ akukhalitsidwanso watsopano tsiku ndi tsiku.
16 Choncho sitikubwerera m’mbuyo. Koma ngakhale munthu wathu wakunja akutha, ndithudi munthu wathu wamkati+ akukhalitsidwanso watsopano tsiku ndi tsiku.