2 Akorinto 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikusonyezanso zimenezi mwa kukhala oyera, odziwa zinthu, oleza mtima,+ okoma mtima,+ okhala ndi mzimu woyera, osonyeza chikondi chopanda chinyengo,+ 1 Atesalonika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.
6 Tikusonyezanso zimenezi mwa kukhala oyera, odziwa zinthu, oleza mtima,+ okoma mtima,+ okhala ndi mzimu woyera, osonyeza chikondi chopanda chinyengo,+
14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.