1 Yohane 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana anga okondedwa,+ tisamakondane ndi mawu okha kapena ndi pakamwa pokha,+ koma tizisonyezana chikondi chenicheni+ m’zochita zathu.+
18 Ana anga okondedwa,+ tisamakondane ndi mawu okha kapena ndi pakamwa pokha,+ koma tizisonyezana chikondi chenicheni+ m’zochita zathu.+