Aroma 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiye chifukwa chake Mulungu anawasiya kuti atsatire zilakolako zamanyazi za kugonana,+ popeza akazi pakati pawo anasiya njira yachibadwa ya matupi awo n’kumachita zosemphana ndi chibadwa.+
26 Ndiye chifukwa chake Mulungu anawasiya kuti atsatire zilakolako zamanyazi za kugonana,+ popeza akazi pakati pawo anasiya njira yachibadwa ya matupi awo n’kumachita zosemphana ndi chibadwa.+