Mateyu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+ Yakobo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakamwa pamodzimodzipo pamatuluka mawu otamanda ndi otemberera. N’kosayenera abale anga kuti zinthu zimenezi zipitirire kuchitika motere.+
11 Chimene chimalowa m’kamwa sichiipitsa munthu, koma chotuluka m’kamwa mwake n’chimene chimaipitsa munthu.”+
10 Pakamwa pamodzimodzipo pamatuluka mawu otamanda ndi otemberera. N’kosayenera abale anga kuti zinthu zimenezi zipitirire kuchitika motere.+