Machitidwe 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mukhale tcheru ndi kuyang’anira+ gulu lonse la nkhosa,+ limene mzimu woyera wakuikani pakati pawo kukhala oyang’anira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi+ a Mwana wake weniweni. Agalatiya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anadzipereka chifukwa cha machimo athu,+ kuti atilanditse ku nthawi* yoipayi,+ mogwirizana ndi chifuniro+ cha Mulungu ndi Atate wathu.
28 Mukhale tcheru ndi kuyang’anira+ gulu lonse la nkhosa,+ limene mzimu woyera wakuikani pakati pawo kukhala oyang’anira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi+ a Mwana wake weniweni.
4 Iye anadzipereka chifukwa cha machimo athu,+ kuti atilanditse ku nthawi* yoipayi,+ mogwirizana ndi chifuniro+ cha Mulungu ndi Atate wathu.