1 Akorinto 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiye chifukwa chake ndikukutumizirani Timoteyo,+ popeza iye ndi mwana wanga wokondedwa ndi wokhulupirika+ mwa Ambuye. Iye adzakukumbutsani mmene ndimachitira zinthu potumikira Khristu Yesu,+ monga mmenenso ineyo ndikuphunzitsira kulikonse, mumpingo uliwonse. 2 Timoteyo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera iwe Timoteyo mwana wanga wokondedwa:+ Kukoma mtima kwakukulu, chifundo, ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi kwa Khristu Yesu Ambuye wathu+ zikhale nawe.
17 Ndiye chifukwa chake ndikukutumizirani Timoteyo,+ popeza iye ndi mwana wanga wokondedwa ndi wokhulupirika+ mwa Ambuye. Iye adzakukumbutsani mmene ndimachitira zinthu potumikira Khristu Yesu,+ monga mmenenso ineyo ndikuphunzitsira kulikonse, mumpingo uliwonse.
2 ndikulembera iwe Timoteyo mwana wanga wokondedwa:+ Kukoma mtima kwakukulu, chifundo, ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi kwa Khristu Yesu Ambuye wathu+ zikhale nawe.