Mateyu 13:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 “Ufumu wakumwamba uli ngati chuma chobisika m’munda, chimene munthu anachipeza n’kuchibisa. Chifukwa cha chimwemwe chimene anali nacho, anapita kukagulitsa+ zinthu zonse zimene anali nazo n’kukagula mundawo.+
44 “Ufumu wakumwamba uli ngati chuma chobisika m’munda, chimene munthu anachipeza n’kuchibisa. Chifukwa cha chimwemwe chimene anali nacho, anapita kukagulitsa+ zinthu zonse zimene anali nazo n’kukagula mundawo.+