1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo. 2 Akorinto 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zoonadi, iye anapachikidwa pamtengo+ chifukwa anadzakhala wofooka,+ koma ali ndi moyo mwa mphamvu ya Mulungu.+ Inde, ifenso ndife ofooka limodzi naye, koma tidzakhala ndi moyo pamodzi naye+ mwa mphamvu ya Mulungu+ imene ikugwira ntchito mwa inu.
4 Zoonadi, iye anapachikidwa pamtengo+ chifukwa anadzakhala wofooka,+ koma ali ndi moyo mwa mphamvu ya Mulungu.+ Inde, ifenso ndife ofooka limodzi naye, koma tidzakhala ndi moyo pamodzi naye+ mwa mphamvu ya Mulungu+ imene ikugwira ntchito mwa inu.