1 Akorinto 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi simukudziwa kuti ochita mpikisano wa liwiro+ amathamanga onse, koma mmodzi yekha ndiye amalandira mphoto?+ Thamangani+ m’njira yoti mukalandire mphotoyo.+
24 Kodi simukudziwa kuti ochita mpikisano wa liwiro+ amathamanga onse, koma mmodzi yekha ndiye amalandira mphoto?+ Thamangani+ m’njira yoti mukalandire mphotoyo.+