Aroma 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho ndikakamaliza zimenezi ndipo ndikakafika bwino ndi zopereka zimenezi+ kwa iwo, ndidzadzera kwanuko popita ku Sipaniya.+
28 Choncho ndikakamaliza zimenezi ndipo ndikakafika bwino ndi zopereka zimenezi+ kwa iwo, ndidzadzera kwanuko popita ku Sipaniya.+