Aroma 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiponso bwanji ngati anachita zimenezo kuti asonyeze kukula kwa ulemerero wake+ kwa ziwiya+ zachifundo, zomwe anazikonzeratu kuti zikhale zaulemerero,+ Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+
23 Ndiponso bwanji ngati anachita zimenezo kuti asonyeze kukula kwa ulemerero wake+ kwa ziwiya+ zachifundo, zomwe anazikonzeratu kuti zikhale zaulemerero,+
7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+