Aroma 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kwa Mulungu wanzeru yekhayo,+ kukhale ulemerero+ kwamuyaya kudzera mwa Yesu Khristu.+ Ame. Agalatiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemu ukhale kwa Mulunguyo mpaka muyaya.+ Ame.