Maliko 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma zina zinagwera panthaka yabwino,+ ndipo zinamera ndi kukula, mwakuti zinayamba kubala zipatso. Mbewu ina inabala zipatso 30, ina 60, ndipo ina 100.”+
8 Koma zina zinagwera panthaka yabwino,+ ndipo zinamera ndi kukula, mwakuti zinayamba kubala zipatso. Mbewu ina inabala zipatso 30, ina 60, ndipo ina 100.”+