Maliko 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Ndipo ngati dzanja lako limakuphunthwitsa, ulidule. Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi, kusiyana n’kupita ku Gehena,* kumoto umene sungazimitsidwe, uli ndi manja onse awiri.+
43 “Ndipo ngati dzanja lako limakuphunthwitsa, ulidule. Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi, kusiyana n’kupita ku Gehena,* kumoto umene sungazimitsidwe, uli ndi manja onse awiri.+