Aroma 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+ Aefeso 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+
18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+
6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+