Aefeso 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatchule ngakhale za khalidwe lochititsa manyazi,+ nkhani zopusa kapena nthabwala zotukwana,+ zomwe ndi zinthu zosayenera. M’malomwake, muziyamika Mulungu.+
4 Musatchule ngakhale za khalidwe lochititsa manyazi,+ nkhani zopusa kapena nthabwala zotukwana,+ zomwe ndi zinthu zosayenera. M’malomwake, muziyamika Mulungu.+