Aefeso 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 sindileka kuyamika Mulungu chifukwa cha inu. Ndikupitirizabe kukutchulani m’mapemphero anga,+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+