Levitiko 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Musamupondereze ndi kumuchitira nkhanza,+ ndipo muziopa Mulungu wanu.+ Deuteronomo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo ukam’masula ndi kumulola kuchoka, usamulole kuchoka chimanjamanja.+