Filimoni 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndikukupempha za mwana wanga+ Onesimo,+ amene ndakhala bambo+ wake pamene ndili m’ndende.