Aroma 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero landiranani,+ monga mmene Khristu anatilandirira,+ kuti ulemerero upite kwa Mulungu.