1 Akorinto 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Popeza pali mkate umodzi, ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri,+ ndife thupi limodzi,+ pakuti tonse tikudya nawo mkate umodziwo.+ Aefeso 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 umene ndi thupi lake.+ Mpingowo ndi wodzaza+ ndi iye, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.+
17 Popeza pali mkate umodzi, ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri,+ ndife thupi limodzi,+ pakuti tonse tikudya nawo mkate umodziwo.+