Aefeso 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+
13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+