Aefeso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 komanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, Khristu akhale m’mitima yanu, pamodzi ndi chikondi+ chimene chiyenera kukhala pakati panu, ndiponso kuti muzike mizu+ ndi kukhala okhazikika pamaziko.+
17 komanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, Khristu akhale m’mitima yanu, pamodzi ndi chikondi+ chimene chiyenera kukhala pakati panu, ndiponso kuti muzike mizu+ ndi kukhala okhazikika pamaziko.+