Aefeso 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse. 1 Atesalonika 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muziyamika+ pa chilichonse, pakuti chimenechi ndi chifuniro cha Mulungu kwa inu mwa Khristu Yesu.
20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse.