Aefeso 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso landirani chisoti cholimba+ chachipulumutso, ndiponso lupanga+ la mzimu,+ lomwe ndilo mawu a Mulungu.+
17 Komanso landirani chisoti cholimba+ chachipulumutso, ndiponso lupanga+ la mzimu,+ lomwe ndilo mawu a Mulungu.+