2 Atesalonika 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho ifeyo timakunyadirani+ ku mipingo ya Mulungu chifukwa cha kupirira kwanu ndi chikhulupiriro chanu pokumana ndi mazunzo ndi masautso onse amene mukulimbana nawo.+
4 Choncho ifeyo timakunyadirani+ ku mipingo ya Mulungu chifukwa cha kupirira kwanu ndi chikhulupiriro chanu pokumana ndi mazunzo ndi masautso onse amene mukulimbana nawo.+